2 Mafumu 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Anagwetsanso chipilala chopatulika cha Baala+ ndi kachisi wa Baala,+ ndipo malowo anawasandutsa zimbudzi+ mpaka lero. Ezara 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndaikanso lamulo lakuti aliyense wophwanya+ lamulo limeneli, thabwa+ lidzazulidwa panyumba yake ndipo iye adzapachikidwa+ pathabwalo. Komanso nyumba yake idzasandutsidwa chimbudzi cha aliyense chifukwa cha zimenezi.+
27 Anagwetsanso chipilala chopatulika cha Baala+ ndi kachisi wa Baala,+ ndipo malowo anawasandutsa zimbudzi+ mpaka lero.
11 Ndaikanso lamulo lakuti aliyense wophwanya+ lamulo limeneli, thabwa+ lidzazulidwa panyumba yake ndipo iye adzapachikidwa+ pathabwalo. Komanso nyumba yake idzasandutsidwa chimbudzi cha aliyense chifukwa cha zimenezi.+