Danieli 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Pambuyo pa zimenezi, ndinaona chilombo china chooneka ngati kambuku*+ koma chinali ndi mapiko anayi a mbalame pamsana pake. Chilombochi chinali ndi mitu inayi+ ndipo chinapatsidwa ulamuliro.
6 “Pambuyo pa zimenezi, ndinaona chilombo china chooneka ngati kambuku*+ koma chinali ndi mapiko anayi a mbalame pamsana pake. Chilombochi chinali ndi mitu inayi+ ndipo chinapatsidwa ulamuliro.