Miyambo 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mkwiyo wa mfumu umatanthauza amithenga a imfa,+ koma munthu wanzeru ndi amene amauziziritsa.+ Miyambo 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mkwiyo wa mfumu uli ngati kubangula kwa mkango wamphamvu,+ koma kukoma mtima kwake kuli ngati mame pazomera.+ Miyambo 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kuopsa kwa mfumu kuli ngati kubangula kwa mkango wamphamvu.+ Aliyense woputa mkwiyo wake akuchimwira moyo wake womwe.+
12 Mkwiyo wa mfumu uli ngati kubangula kwa mkango wamphamvu,+ koma kukoma mtima kwake kuli ngati mame pazomera.+
2 Kuopsa kwa mfumu kuli ngati kubangula kwa mkango wamphamvu.+ Aliyense woputa mkwiyo wake akuchimwira moyo wake womwe.+