Maliro 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova wachita zimene anali kuganiza.+ Wakwaniritsa zimene ananena,+Zimene analamula kalekale.+ Wapasula zinthu ndipo sanamve chisoni.+Wachititsa adani ako kusangalala+ chifukwa cha zimene zakuchitikira. Wakweza nyanga ya adani+ ako.
17 Yehova wachita zimene anali kuganiza.+ Wakwaniritsa zimene ananena,+Zimene analamula kalekale.+ Wapasula zinthu ndipo sanamve chisoni.+Wachititsa adani ako kusangalala+ chifukwa cha zimene zakuchitikira. Wakweza nyanga ya adani+ ako.