1 Mafumu 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Maso anu akhale akuyang’ana+ nyumba ino usiku ndi usana. Akhale akuyang’ana malo amene munanena kuti, ‘Dzina langa lidzakhala kumeneko,’+ kuti mumvere pemphero limene mtumiki wanu akupemphera atayang’ana kumalo ano.+ Salimo 17:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ine ndikuitana pa inu, chifukwa mudzandiyankha, inu Mulungu.+Tcherani khutu kwa ine. Imvani mawu anga.+
29 Maso anu akhale akuyang’ana+ nyumba ino usiku ndi usana. Akhale akuyang’ana malo amene munanena kuti, ‘Dzina langa lidzakhala kumeneko,’+ kuti mumvere pemphero limene mtumiki wanu akupemphera atayang’ana kumalo ano.+
6 Ine ndikuitana pa inu, chifukwa mudzandiyankha, inu Mulungu.+Tcherani khutu kwa ine. Imvani mawu anga.+