Yesaya 64:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tonsefe takhala ngati munthu wodetsedwa, ndipo zochita zathu zonse zolungama zili ngati kansalu kamene mkazi amavala pa nthawi yosamba.+ Tonsefe tidzayoyoka ngati masamba+ ndipo zolakwa zathu zidzatiuluzira kutali ngati mphepo.+ Yeremiya 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngakhale kuti zolakwa zathu n’zoonekeratu, inu Yehova, chitanipo kanthu chifukwa cha dzina lanu,+ pakuti zochita zathu zosonyeza kusakhulupirika zachuluka+ ndipo takuchimwirani.+
6 Tonsefe takhala ngati munthu wodetsedwa, ndipo zochita zathu zonse zolungama zili ngati kansalu kamene mkazi amavala pa nthawi yosamba.+ Tonsefe tidzayoyoka ngati masamba+ ndipo zolakwa zathu zidzatiuluzira kutali ngati mphepo.+
7 Ngakhale kuti zolakwa zathu n’zoonekeratu, inu Yehova, chitanipo kanthu chifukwa cha dzina lanu,+ pakuti zochita zathu zosonyeza kusakhulupirika zachuluka+ ndipo takuchimwirani.+