Salimo 79:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Musatiimbe mlandu chifukwa cha zolakwa za makolo athu.+Fulumirani! Tisonyezeni chifundo chanu,+Chifukwa tasautsika koopsa.+
8 Musatiimbe mlandu chifukwa cha zolakwa za makolo athu.+Fulumirani! Tisonyezeni chifundo chanu,+Chifukwa tasautsika koopsa.+