Yesaya 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndinati: “Tsoka kwa ine! Popeza maso anga aona Mfumu, Yehova wa makamu.+ Nditsikira kuli chete pakuti ndine munthu wa milomo yodetsedwa,+ ndipo ndikukhala pakati pa anthu a milomo yodetsedwa.”+
5 Ine ndinati: “Tsoka kwa ine! Popeza maso anga aona Mfumu, Yehova wa makamu.+ Nditsikira kuli chete pakuti ndine munthu wa milomo yodetsedwa,+ ndipo ndikukhala pakati pa anthu a milomo yodetsedwa.”+