Yohane 3:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Amene walandira umboni wakewo waika chisindikizo chake pa umboniwo chakuti Mulungu amanena zoona.+ 2 Akorinto 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiponso malonjezo a Mulungu, kaya akhale ochuluka chotani,+ akhala Inde kudzera mwa iye.+ Choteronso kudzera mwa iye, “Ame”+ amanenedwa kwa Mulungu kuti Mulungu alandire ulemerero kudzera mwa ife.
33 Amene walandira umboni wakewo waika chisindikizo chake pa umboniwo chakuti Mulungu amanena zoona.+
20 Ndiponso malonjezo a Mulungu, kaya akhale ochuluka chotani,+ akhala Inde kudzera mwa iye.+ Choteronso kudzera mwa iye, “Ame”+ amanenedwa kwa Mulungu kuti Mulungu alandire ulemerero kudzera mwa ife.