Genesis 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Dzina la mtsinje wachitatu ndi Hidekeli,+ umene umalowera kum’mawa kwa Asuri.+ Ndipo mtsinje wachinayi ndi Firate.+
14 Dzina la mtsinje wachitatu ndi Hidekeli,+ umene umalowera kum’mawa kwa Asuri.+ Ndipo mtsinje wachinayi ndi Firate.+