1 Samueli 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako Yehova anabwera ndi kuima pamalopo n’kuitananso ngati poyamba paja, kuti: “Samueli, Samueli!” Poyankha Samueli anati: “Lankhulani, ine mtumiki wanu ndikumvetsera.”+
10 Kenako Yehova anabwera ndi kuima pamalopo n’kuitananso ngati poyamba paja, kuti: “Samueli, Samueli!” Poyankha Samueli anati: “Lankhulani, ine mtumiki wanu ndikumvetsera.”+