Salimo 36:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ali pabedi lake amakonza chiwembu kuti apweteke anzake.+Amaima panjira yoipa.+Sapewa kuchita zinthu zoipa.+ Miyambo 6:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 mtima wokonzera ena ziwembu,+ mapazi othamangira kukachita zoipa,+
4 Ali pabedi lake amakonza chiwembu kuti apweteke anzake.+Amaima panjira yoipa.+Sapewa kuchita zinthu zoipa.+