Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 7:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Masiku ako akadzakwana,+ ndipo ukadzagona pamodzi ndi makolo ako,+ pamenepo ndidzautsa mbewu yako yobwera pambuyo pako, imene idzatuluka m’chiuno mwako. Ndipo ndidzakhazikitsadi ufumu wake.+

  • 2 Samueli 23:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Kodi si mmene nyumba yanga ilili kwa Mulungu?+

      Chifukwa chakuti anachita nane pangano lomwe lidzakhalapo mpaka kalekale,+

      Analikonza bwino ndipo n’lotetezeka.+

      Chifukwa ndilo chipulumutso changa+ ndi chondikondweretsa,

      Kodi chimenechi sindicho chifukwa chake adzakulitsa panganoli?+

  • Salimo 89:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ndidzamusonyeza kukoma mtima kwanga kosatha mpaka kalekale,+

      Ndipo pangano limene ndinachita naye silidzaphwanyidwa.+

  • Luka 1:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Iye adzalamulira monga mfumu panyumba ya Yakobo kwamuyaya, moti ufumu wake sudzatha konse.”+

  • Luka 22:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Choncho ndikuchita nanu pangano,+ mmene Atate wanga wachitira pangano la ufumu ndi ine,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena