Genesis 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ana a Yavani anali Elisaha,+ Tarisi,+ Kitimu+ ndi Dodanimu.+ Numeri 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Padzafika zombo zochokera kugombe la Kitimu,+Ndipo iwo adzasautsa Asuri+ ndithu,Adzasautsadi Ebere.Koma iyenso adzawonongeka pamapeto pake.” Yesaya 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Uthenga wokhudza Turo:+ Lirani mofuula inu zombo za ku Tarisi,+ chifukwa chakuti mzindawo wasakazidwa ndipo sulinso doko. Sulinso malo oti mungafikepo.+ Anthu amva zimenezi ali kudziko la Kitimu.+ Yeremiya 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘Wolokerani ku Kitimu,+ m’mbali mwa nyanja, kuti muone. Tumizani anthu ku Kedara+ ndipo muganizire bwinobwino kuti muone ngati zoterezi zinachitikapo kumeneko.+ Ezekieli 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Zopalasira ngalawa zako anazipanga ndi mitengo ikuluikulu ya ku Basana. Mbali ya kutsogolo kwako anaipanga ndi matabwa a paini, n’kuikongoletsa ndi minyanga yochokera kuzilumba za Kitimu.+
24 Padzafika zombo zochokera kugombe la Kitimu,+Ndipo iwo adzasautsa Asuri+ ndithu,Adzasautsadi Ebere.Koma iyenso adzawonongeka pamapeto pake.”
23 Uthenga wokhudza Turo:+ Lirani mofuula inu zombo za ku Tarisi,+ chifukwa chakuti mzindawo wasakazidwa ndipo sulinso doko. Sulinso malo oti mungafikepo.+ Anthu amva zimenezi ali kudziko la Kitimu.+
10 “‘Wolokerani ku Kitimu,+ m’mbali mwa nyanja, kuti muone. Tumizani anthu ku Kedara+ ndipo muganizire bwinobwino kuti muone ngati zoterezi zinachitikapo kumeneko.+
6 Zopalasira ngalawa zako anazipanga ndi mitengo ikuluikulu ya ku Basana. Mbali ya kutsogolo kwako anaipanga ndi matabwa a paini, n’kuikongoletsa ndi minyanga yochokera kuzilumba za Kitimu.+