Danieli 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mfumu yobwera kudzamenyana nayo* idzachita zofuna zake, ndipo palibe adzaime pamaso pake. Mfumuyo idzaimirira m’Dziko Lokongola,+ ndipo idzapha anthu ambiri.+
16 Mfumu yobwera kudzamenyana nayo* idzachita zofuna zake, ndipo palibe adzaime pamaso pake. Mfumuyo idzaimirira m’Dziko Lokongola,+ ndipo idzapha anthu ambiri.+