Luka 18:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Koma iwo sanamvetse tanthauzo la chilichonse cha zimenezi. Mawu amenewa anabisika kwa iwo, ndipo sanadziwe zimene zinanenedwazo.+ Machitidwe 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anawayankha kuti: “Si kwa inu kudziwa nthawi kapena nyengo+ zimene Atate waziika pansi pa ulamuliro wake.+ 1 Petulo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anali kufufuza nyengo+ yake kapena mtundu wa nyengo imene mzimu+ umene unali mwa iwo unali kuwasonyeza yokhudzana ndi Khristu.+ Mzimuwo unali kuchitira umboni za masautso a Khristu+ ndi za ulemerero+ wobwera pambuyo pake.
34 Koma iwo sanamvetse tanthauzo la chilichonse cha zimenezi. Mawu amenewa anabisika kwa iwo, ndipo sanadziwe zimene zinanenedwazo.+
7 Iye anawayankha kuti: “Si kwa inu kudziwa nthawi kapena nyengo+ zimene Atate waziika pansi pa ulamuliro wake.+
11 Anali kufufuza nyengo+ yake kapena mtundu wa nyengo imene mzimu+ umene unali mwa iwo unali kuwasonyeza yokhudzana ndi Khristu.+ Mzimuwo unali kuchitira umboni za masautso a Khristu+ ndi za ulemerero+ wobwera pambuyo pake.