Danieli 2:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mutu wa chifaniziro chimenechi unali wopangidwa ndi golide wabwino,+ chifuwa chake ndi manja ake zinali zasiliva,+ mimba yake ndi ntchafu zake zinali zamkuwa,+ Danieli 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Masamba ake anali okongola ndipo unali ndi zipatso zambiri. Mumtengomo munali zakudya zokwanira chamoyo chilichonse. Nyama zakutchire zinali kukhala pansi pake.+ Mbalame zam’mlengalenga zinali kukhala panthambi zake.
32 Mutu wa chifaniziro chimenechi unali wopangidwa ndi golide wabwino,+ chifuwa chake ndi manja ake zinali zasiliva,+ mimba yake ndi ntchafu zake zinali zamkuwa,+
21 Masamba ake anali okongola ndipo unali ndi zipatso zambiri. Mumtengomo munali zakudya zokwanira chamoyo chilichonse. Nyama zakutchire zinali kukhala pansi pake.+ Mbalame zam’mlengalenga zinali kukhala panthambi zake.