Yesaya 42:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu amene akudalira zifaniziro zosema, amene akuuza zifaniziro zopangidwa ndi chitsulo chosungunula kuti: “Ndinu milungu yathu,” adzathawa ndipo adzachita manyazi kwambiri.+ Yeremiya 2:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Monga mmene mbala imachitira manyazi ikagwidwa, anthu a m’nyumba ya Isiraeli nawonso achita manyazi,+ iwowo, mafumu awo, akalonga awo, ansembe awo ndiponso aneneri awo.+
17 Anthu amene akudalira zifaniziro zosema, amene akuuza zifaniziro zopangidwa ndi chitsulo chosungunula kuti: “Ndinu milungu yathu,” adzathawa ndipo adzachita manyazi kwambiri.+
26 “Monga mmene mbala imachitira manyazi ikagwidwa, anthu a m’nyumba ya Isiraeli nawonso achita manyazi,+ iwowo, mafumu awo, akalonga awo, ansembe awo ndiponso aneneri awo.+