Miyambo 30:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pali m’badwo umene maso ake ali pamwamba kwambiri, ndiponso umene maso ake owala ali odzikweza.+ Yesaya 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mawu onsewa anthu adzawadziwa.+ Efuraimu ndi anthu okhala ku Samariya,+ adzawadziwa mawuwo chifukwa cha kudzikweza kwawo ndiponso chifukwa cha mwano wa mumtima mwawo. Pakuti iwo anena kuti:+ Hoseya 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kunyada kwa Isiraeli kwakhala umboni womutsutsa,+ koma iwo sanabwerere kwa Yehova Mulungu wawo.+ Sanamufunefune ngakhale kuti achita zinthu zonsezi.+
9 Mawu onsewa anthu adzawadziwa.+ Efuraimu ndi anthu okhala ku Samariya,+ adzawadziwa mawuwo chifukwa cha kudzikweza kwawo ndiponso chifukwa cha mwano wa mumtima mwawo. Pakuti iwo anena kuti:+
10 Kunyada kwa Isiraeli kwakhala umboni womutsutsa,+ koma iwo sanabwerere kwa Yehova Mulungu wawo.+ Sanamufunefune ngakhale kuti achita zinthu zonsezi.+