Deuteronomo 4:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pamapeto pake, mawu amenewa akadzakwaniritsidwa pa inu, n’kukhala pamavuto aakulu, mudzabwereradi kwa Yehova Mulungu wanu+ ndi kumvetsera mawu ake.+ 1 Samueli 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo amuna a Isiraeli anaona kuti zinthu zawathina,+ chifukwa anthu onse anali atapanikizika. Anthuwo anapita kukabisala m’mapanga,+ m’maenje, kumatanthwe, m’zipinda za pansi ndi m’zitsime zopanda madzi.
30 Pamapeto pake, mawu amenewa akadzakwaniritsidwa pa inu, n’kukhala pamavuto aakulu, mudzabwereradi kwa Yehova Mulungu wanu+ ndi kumvetsera mawu ake.+
6 Ndipo amuna a Isiraeli anaona kuti zinthu zawathina,+ chifukwa anthu onse anali atapanikizika. Anthuwo anapita kukabisala m’mapanga,+ m’maenje, kumatanthwe, m’zipinda za pansi ndi m’zitsime zopanda madzi.