Miyambo 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mumtima mwake muli zopotoka.+ Nthawi zonse amakhala akukonza zoipa.+ Amakhalira kuyambanitsa anthu.+ Nahumu 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kodi anthu inu mungakonze chiwembu chotani kuti muukire Yehova?+ Iye adzakufafanizani moti simudzakhalaponso. Sipadzakhalanso nsautso.+
14 Mumtima mwake muli zopotoka.+ Nthawi zonse amakhala akukonza zoipa.+ Amakhalira kuyambanitsa anthu.+
9 Kodi anthu inu mungakonze chiwembu chotani kuti muukire Yehova?+ Iye adzakufafanizani moti simudzakhalaponso. Sipadzakhalanso nsautso.+