Yeremiya 43:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye adzaphwanyaphwanya zipilala za ku Beti-semesi,* mzinda umene uli ku Iguputo. Ndipo nyumba za milungu ya Iguputo adzazitentha.”’” Mika 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndidzagwetsa zifaniziro zanu zogoba ndi zipilala zopatulika zimene zili pakati panu, ndipo simudzagwadiranso ntchito za manja anu.+ Zekariya 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova wa makamu wanena kuti, “Pa tsiku limenelo, ndidzathetsa mayina a mafano m’dziko lonseli+ ndipo mafanowo sadzakumbukiridwanso. M’dzikoli ndidzachotsamo aneneri+ komanso mzimu wonyansa.+
13 Iye adzaphwanyaphwanya zipilala za ku Beti-semesi,* mzinda umene uli ku Iguputo. Ndipo nyumba za milungu ya Iguputo adzazitentha.”’”
13 Ndidzagwetsa zifaniziro zanu zogoba ndi zipilala zopatulika zimene zili pakati panu, ndipo simudzagwadiranso ntchito za manja anu.+
2 Yehova wa makamu wanena kuti, “Pa tsiku limenelo, ndidzathetsa mayina a mafano m’dziko lonseli+ ndipo mafanowo sadzakumbukiridwanso. M’dzikoli ndidzachotsamo aneneri+ komanso mzimu wonyansa.+