2 Mafumu 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye ndiye amene Salimanesere+ mfumu ya Asuri+ anabwera kudzamuthira nkhondo. Chotero Hoshiya anakhala mtumiki wake n’kuyamba kupereka msonkho+ kwa iye. Hoseya 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 “Efuraimu anaona kudwala kwake ndipo Yuda anaona chilonda chake.+ Pamenepo Efuraimu anapita ku Asuri+ ndipo anatumiza amithenga kwa mfumu yaikulu.+ Koma mfumuyo sinathe kukuchiritsani anthu inu,+ ndipo sinathe kupoletsa chilonda chanu.+
3 Iye ndiye amene Salimanesere+ mfumu ya Asuri+ anabwera kudzamuthira nkhondo. Chotero Hoshiya anakhala mtumiki wake n’kuyamba kupereka msonkho+ kwa iye.
13 “Efuraimu anaona kudwala kwake ndipo Yuda anaona chilonda chake.+ Pamenepo Efuraimu anapita ku Asuri+ ndipo anatumiza amithenga kwa mfumu yaikulu.+ Koma mfumuyo sinathe kukuchiritsani anthu inu,+ ndipo sinathe kupoletsa chilonda chanu.+