2 Mafumu 17:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye ndiye amene Salimanesere+ mfumu ya Asuri+ anabwera kudzamuthira nkhondo. Chotero Hoshiya anakhala mtumiki wake n’kuyamba kupereka msonkho+ kwa iye.
3 Iye ndiye amene Salimanesere+ mfumu ya Asuri+ anabwera kudzamuthira nkhondo. Chotero Hoshiya anakhala mtumiki wake n’kuyamba kupereka msonkho+ kwa iye.