Yesaya 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye adzakwezera chizindikiro mitundu ya anthu n’kusonkhanitsa Aisiraeli omwe anamwazikana.+ Ndipo adzasonkhanitsa pamodzi Ayuda omwe anabalalika, kuchokera kumalekezero anayi a dziko lapansi.+ Yesaya 60:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Kodi amene akubwera chouluka ngati mtambowa ndani?+ Ndani awa akubwera ngati nkhunda zimene zikuulukira kumakomo a makola awo?
12 Iye adzakwezera chizindikiro mitundu ya anthu n’kusonkhanitsa Aisiraeli omwe anamwazikana.+ Ndipo adzasonkhanitsa pamodzi Ayuda omwe anabalalika, kuchokera kumalekezero anayi a dziko lapansi.+
8 “Kodi amene akubwera chouluka ngati mtambowa ndani?+ Ndani awa akubwera ngati nkhunda zimene zikuulukira kumakomo a makola awo?