Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 17:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamalo okwezeka onsewo, iwo anapitiriza kufukizapo nsembe yautsi, mofanana ndi mitundu+ imene Yehova anaithamangitsa m’dzikolo chifukwa cha Aisiraeliwo. Iwo anapitiriza kuchita zinthu zoipa zokwiyitsa+ Yehova.

  • Ezekieli 23:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Ohola anayamba kuchita uhule+ ngakhale kuti anali mkazi wanga. Anali kulakalaka kwambiri amuna amene ankakhumba kugona naye.+ Anali kulakalaka Asuri+ amene anali kukhala moyandikana naye.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena