Yeremiya 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu inu, funsani kuti mudziwe ngati mwamuna angabale mwana.+ N’chifukwa chiyani mwamuna aliyense wamphamvu akuoneka atagwira manja m’chiuno ngati mkazi amene akubala mwana? N’chifukwa chiyani nkhope zawo zonse zafooka?+ Mika 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Tsopano n’chifukwa chiyani ukufuula kwambiri?+ Kodi mwa iwe mulibe mfumu, kapena kodi alangizi ako awonongedwa? Kodi n’chifukwa chake zowawa ngati za mkazi amene akubereka zakugwira?+
6 Anthu inu, funsani kuti mudziwe ngati mwamuna angabale mwana.+ N’chifukwa chiyani mwamuna aliyense wamphamvu akuoneka atagwira manja m’chiuno ngati mkazi amene akubala mwana? N’chifukwa chiyani nkhope zawo zonse zafooka?+
9 “Tsopano n’chifukwa chiyani ukufuula kwambiri?+ Kodi mwa iwe mulibe mfumu, kapena kodi alangizi ako awonongedwa? Kodi n’chifukwa chake zowawa ngati za mkazi amene akubereka zakugwira?+