Yesaya 17:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Masana ukhoza kuumangira mpanda wabwino munda wakowo, ndipo m’mawa ukhoza kuchititsa mbewu yako kuti iphuke. Koma zokolola zake zidzathawa m’tsiku la matenda ndi ululu wosachiritsika.+ Ezekieli 16:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Tsopano ine ndidzakutambasulira dzanja langa+ ndipo ndidzakuchepetsera gawo lako.+ Ndidzakupereka ku zilakolako+ za akazi odana nawe,+ ana aakazi a Afilisiti,+ akazi amene akuchita manyazi ndi khalidwe lako lotayirira.+
11 Masana ukhoza kuumangira mpanda wabwino munda wakowo, ndipo m’mawa ukhoza kuchititsa mbewu yako kuti iphuke. Koma zokolola zake zidzathawa m’tsiku la matenda ndi ululu wosachiritsika.+
27 Tsopano ine ndidzakutambasulira dzanja langa+ ndipo ndidzakuchepetsera gawo lako.+ Ndidzakupereka ku zilakolako+ za akazi odana nawe,+ ana aakazi a Afilisiti,+ akazi amene akuchita manyazi ndi khalidwe lako lotayirira.+