Ezekieli 23:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Adzakuvula zovala zako+ ndi kutenga zinthu zako zokongola.+ Zefaniya 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chuma chawo chidzafunkhidwa ndipo nyumba zawo zidzakhala bwinja.+ Iwo adzamanga nyumba, koma sadzakhalamo.+ Iwo adzalima minda ya mpesa koma sadzamwa vinyo wochokera mmenemo.+
13 Chuma chawo chidzafunkhidwa ndipo nyumba zawo zidzakhala bwinja.+ Iwo adzamanga nyumba, koma sadzakhalamo.+ Iwo adzalima minda ya mpesa koma sadzamwa vinyo wochokera mmenemo.+