Deuteronomo 21:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Azisintha chovala chimene anavala pamene anali kugwidwa ndipo akhale m’nyumba mwako ndi kulira maliro a bambo ake ndi a mayi ake kwa mwezi wathunthu.+ Kenako umutenge kukhala mkazi wako. Akhale mkwatibwi wako ndipo ugone naye.
13 Azisintha chovala chimene anavala pamene anali kugwidwa ndipo akhale m’nyumba mwako ndi kulira maliro a bambo ake ndi a mayi ake kwa mwezi wathunthu.+ Kenako umutenge kukhala mkazi wako. Akhale mkwatibwi wako ndipo ugone naye.