Aroma 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ngati angakwatiwe ndi mwamuna wina, mwamuna wake ali moyo, mkaziyo adzatchedwa wachigololo.+ Koma ngati mwamuna wake wamwalira, mkaziyo wamasuka ku lamulo lake, chotero si wachigololo ngati atakwatiwa ndi mwamuna wina.+
3 Ngati angakwatiwe ndi mwamuna wina, mwamuna wake ali moyo, mkaziyo adzatchedwa wachigololo.+ Koma ngati mwamuna wake wamwalira, mkaziyo wamasuka ku lamulo lake, chotero si wachigololo ngati atakwatiwa ndi mwamuna wina.+