Salimo 49:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Mvetserani izi, anthu nonsenu.Tcherani khutu inu nonse a m’nthawi* ino,+ Amosi 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Tamverani mawu amene Yehova wanena okhudza inu+ ana Aisiraeli, mawu okhudza banja lonse limene ndinalitulutsa m’dziko la Iguputo.+ Mawuwo ndi akuti,
49 Mvetserani izi, anthu nonsenu.Tcherani khutu inu nonse a m’nthawi* ino,+ Amosi 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Tamverani mawu amene Yehova wanena okhudza inu+ ana Aisiraeli, mawu okhudza banja lonse limene ndinalitulutsa m’dziko la Iguputo.+ Mawuwo ndi akuti,
3 “Tamverani mawu amene Yehova wanena okhudza inu+ ana Aisiraeli, mawu okhudza banja lonse limene ndinalitulutsa m’dziko la Iguputo.+ Mawuwo ndi akuti,