Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 51:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Mwana wamkazi wa Babulo ali ngati malo opunthira mbewu.+ Ino ndi nthawi yomupondaponda. Koma kwatsala ka nthawi pang’ono kuti nthawi yokolola imufikire.”+

  • Chivumbulutso 14:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndipo mngelo winanso anatuluka kuguwa lansembe. Iyeyu anali ndi ulamuliro pa moto.+ Anafuula kwa mngelo amene anali ndi chikwakwa chakuthwa uja ndi mawu okweza, akuti: “Tsitsa chikwakwa chako chakuthwacho umwete mpesa wa padziko lapansi,+ ndi kusonkhanitsa pamodzi masango a mphesa zake, chifukwa mphesa zakezo zapsa.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena