Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 63:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Moponderamo mphesa ndapondapondamo ndekha,+ chifukwa palibe munthu amene anali nane wochokera pakati pa mitundu ya anthu. Iwo ndawapondaponda mu mkwiyo wanga,+ ndipo ndawapondereza mu ukali wanga.+ Magazi awo awazikira pazovala zanga,+ ndipo ndaipitsa zovala zanga zonse.

  • Maliro 1:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Yehova wandichotsera anthu anga onse amphamvu+ ndi kuwakankhira pambali.

      Wandiitanitsira msonkhano kuti athyolethyole anyamata anga.+

      Yehova wapondaponda moponderamo mphesa+ mwa namwali, mwana wamkazi wa Yuda.+

  • Chivumbulutso 14:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndipo anapondaponda mopondera mphesamo kunja kwa mzinda,+ ndipo magazi anatuluka m’choponderamo mphesacho mpaka kufika m’zibwano za mahatchi,+ n’kuyenderera mtunda wa masitadiya 1,600.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena