Levitiko 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “‘Munthu akafuna kupereka nsembe yambewu+ kwa Yehova, nsembe yakeyo izikhala ufa wosalala.+ Azithira mafuta ndi kuika lubani* pa ufawo. Yoweli 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndani akudziwa kuti mwina adzasintha maganizo ake ndi kukumverani chisoni+ ndipo kenako adzakusiyirani madalitso,+ nsembe yambewu ndi nsembe yachakumwa kuti mupereke kwa Yehova Mulungu wanu?
2 “‘Munthu akafuna kupereka nsembe yambewu+ kwa Yehova, nsembe yakeyo izikhala ufa wosalala.+ Azithira mafuta ndi kuika lubani* pa ufawo.
14 Ndani akudziwa kuti mwina adzasintha maganizo ake ndi kukumverani chisoni+ ndipo kenako adzakusiyirani madalitso,+ nsembe yambewu ndi nsembe yachakumwa kuti mupereke kwa Yehova Mulungu wanu?