Salimo 48:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ife taona zimene Mulungu anachita monga mmene tinamvera,+Mumzinda wa Yehova wa makamu, mumzinda wa Mulungu wathu.+Mulungu adzakhazikitsa mzindawo mpaka kalekale.+ [Seʹlah.] Yesaya 60:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “M’malo mokhala wosiyidwa mpaka kalekale ndi wodedwa, popanda aliyense wodutsa mwa iwe,+ ine ndidzakuika monga chinthu chonyaditsa mpaka kalekale, ndiponso chinthu chokondweretsa ku mibadwomibadwo.+ Amosi 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “‘Ine ndidzawabzala panthaka yawo ndipo sadzazulidwanso m’dziko limene ndawapatsa,’+ watero Yehova Mulungu wanu.”
8 Ife taona zimene Mulungu anachita monga mmene tinamvera,+Mumzinda wa Yehova wa makamu, mumzinda wa Mulungu wathu.+Mulungu adzakhazikitsa mzindawo mpaka kalekale.+ [Seʹlah.]
15 “M’malo mokhala wosiyidwa mpaka kalekale ndi wodedwa, popanda aliyense wodutsa mwa iwe,+ ine ndidzakuika monga chinthu chonyaditsa mpaka kalekale, ndiponso chinthu chokondweretsa ku mibadwomibadwo.+
15 “‘Ine ndidzawabzala panthaka yawo ndipo sadzazulidwanso m’dziko limene ndawapatsa,’+ watero Yehova Mulungu wanu.”