2 Mbiri 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nthawi yonseyi anthu onse a ku Yuda anali ataimirira pamaso pa Yehova,+ kuphatikizapo akazi awo ndi ana awo, ngakhalenso ana awo ang’onoang’ono.+ Nehemiya 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pa tsiku la 24 la mwezi umenewu+ ana a Isiraeli anasonkhana pamodzi. Iwo anali kusala kudya+ atavala ziguduli*+ ndiponso atadzithira dothi+ kumutu.
13 Nthawi yonseyi anthu onse a ku Yuda anali ataimirira pamaso pa Yehova,+ kuphatikizapo akazi awo ndi ana awo, ngakhalenso ana awo ang’onoang’ono.+
9 Pa tsiku la 24 la mwezi umenewu+ ana a Isiraeli anasonkhana pamodzi. Iwo anali kusala kudya+ atavala ziguduli*+ ndiponso atadzithira dothi+ kumutu.