Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 13:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Fuulani, anthu inu,+ chifukwa tsiku la Yehova lili pafupi.+ Lidzabwera ngati kuti Wamphamvuyonse akulanda zinthu.+

  • Yoweli 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Lizani lipenga m’Ziyoni+ amuna inu ndipo fuulani mfuu yankhondo+ m’phiri langa loyera.+ Anthu onse okhala m’dzikoli anjenjemere,+ pakuti tsiku la Yehova likubwera+ ndipo lili pafupi!

  • Zefaniya 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Khalani chete pamaso pa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa,+ pakuti tsiku la Yehova lili pafupi,+ ndipo Yehova wakonza nsembe+ moti wakonzekeretsa*+ anthu amene wawaitana.

  • Zefaniya 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Tsiku lalikulu+ la Yehova lili pafupi.+ Lili pafupi ndipo likubwera mofulumira kwambiri.+ Mkokomo wa tsiku la Yehova ukubwera ndi zowawa.+ Pa tsiku limenelo mwamuna wamphamvu adzalira.+

  • Zefaniya 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Lamulo lisanayambe kugwira ntchito,+ tsiku lisanadutse ngati mankhusu,* mkwiyo woyaka moto wa Yehova usanakugwereni anthu inu,+ tsiku la mkwiyo wa Yehova lisanakufikireni,+

  • 2 Petulo 3:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Komabe, tsiku la Yehova+ lidzafika ngati mbala,+ pamene kumwamba kudzachoka+ ndi mkokomo waukulu,+ koma zinthu zimene zimapanga kumwamba ndi dziko lapansi zidzatentha kwambiri n’kusungunuka,+ ndipo dziko lapansi+ ndi ntchito zake zidzaonekera poyera.+

  • Chivumbulutso 6:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 chifukwa tsiku lalikulu+ la mkwiyo wawo+ lafika, ndipo ndani angaimirire pamaso pawo?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena