Deuteronomo 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kumalo amenewo, inuyo ndi mabanja anu muzidzadya zimenezi ndi kusangalala ndi zochita zanu zonse+ pamaso pa Yehova,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu wakudalitsani.
7 Kumalo amenewo, inuyo ndi mabanja anu muzidzadya zimenezi ndi kusangalala ndi zochita zanu zonse+ pamaso pa Yehova,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu wakudalitsani.