Yeremiya 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pachifukwa chimenechi dziko lidzalira+ ndipo kumwamba kudzachita mdima.+ Izi zili choncho chifukwa ndanena, ndaganiza zimenezi mozama, sindinadziimbe mlandu ndipo sindisintha maganizo anga.+ Yeremiya 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Patsani Yehova Mulungu wanu ulemerero+ asanachititse mdima,+ komanso mapazi anu asanapunthwe pamapiri madzulo dzuwa litalowa.+ Mudzayembekeza kuwala+ koma iye adzabweretsa mdima,+ ndipo adzachititsa mdima wandiweyani.+ Amosi 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Tsoka kwa anthu amene akulakalaka tsiku la Yehova!+ Kodi mukuyembekezera chiyani pa tsiku la Yehova anthu inu?+ Limeneli lidzakhala tsiku lamdima osati kuwala,+
28 Pachifukwa chimenechi dziko lidzalira+ ndipo kumwamba kudzachita mdima.+ Izi zili choncho chifukwa ndanena, ndaganiza zimenezi mozama, sindinadziimbe mlandu ndipo sindisintha maganizo anga.+
16 Patsani Yehova Mulungu wanu ulemerero+ asanachititse mdima,+ komanso mapazi anu asanapunthwe pamapiri madzulo dzuwa litalowa.+ Mudzayembekeza kuwala+ koma iye adzabweretsa mdima,+ ndipo adzachititsa mdima wandiweyani.+
18 “‘Tsoka kwa anthu amene akulakalaka tsiku la Yehova!+ Kodi mukuyembekezera chiyani pa tsiku la Yehova anthu inu?+ Limeneli lidzakhala tsiku lamdima osati kuwala,+