Ekisodo 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndipo dzombelo linayamba kufika m’dziko lonse la Iguputo ndi kutera m’madera onse a dzikolo.+ Linawasautsa kwambiri.+ Dzombe ngati limeneli linali lisanagwepo n’kale lonse ndipo sipadzagwanso lina ngati limeneli.
14 Ndipo dzombelo linayamba kufika m’dziko lonse la Iguputo ndi kutera m’madera onse a dzikolo.+ Linawasautsa kwambiri.+ Dzombe ngati limeneli linali lisanagwepo n’kale lonse ndipo sipadzagwanso lina ngati limeneli.