Yoweli 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Ine ndidzaitana inu Yehova,+ pakuti moto wawononga malo odyetserako ziweto m’chipululu ndipo moto walawilawi wanyeketsa mitengo yonse yakuthengo.+
19 “Ine ndidzaitana inu Yehova,+ pakuti moto wawononga malo odyetserako ziweto m’chipululu ndipo moto walawilawi wanyeketsa mitengo yonse yakuthengo.+