Amosi 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, anandionetsanso masomphenya awa: Ndinaona Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, akuuza anthu ake kuti alimbane naye pogwiritsira ntchito moto.+ Motowo unaumitsa madzi akuya ndiponso unawononga kachigawo ka dziko.
4 Kenako, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, anandionetsanso masomphenya awa: Ndinaona Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, akuuza anthu ake kuti alimbane naye pogwiritsira ntchito moto.+ Motowo unaumitsa madzi akuya ndiponso unawononga kachigawo ka dziko.