Yeremiya 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova wanena kuti: “Ngati ungabwerere, iwe Isiraeli, ubwerere kwa ine.+ Ndipo ngati ungachotse zinthu zako zonyansazo chifukwa cha ine,+ sudzakhalanso wothawathawa. Hoseya 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Koma iwe ubwerere kwa Mulungu wako.+ Usonyeze kukoma mtima kosatha+ ndi chilungamo+ ndipo nthawi zonse uziyembekezera Mulungu wako.+ Hoseya 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Iwe Isiraeli, bwerera kwa Yehova Mulungu wako+ pakuti wapunthwa mu zolakwa zako.+
4 Yehova wanena kuti: “Ngati ungabwerere, iwe Isiraeli, ubwerere kwa ine.+ Ndipo ngati ungachotse zinthu zako zonyansazo chifukwa cha ine,+ sudzakhalanso wothawathawa.
6 “Koma iwe ubwerere kwa Mulungu wako.+ Usonyeze kukoma mtima kosatha+ ndi chilungamo+ ndipo nthawi zonse uziyembekezera Mulungu wako.+