Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 14:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 ‘Yehova ndi wosakwiya msanga,+ ndipo ndi wodzaza ndi kukoma mtima kosatha.+ Amakhululukira wolakwa ndi wophwanya malamulo,+ koma iye salekerera konse wolakwa osam’langa.+ Amalanga ana, zidzukulu, ndi ana a zidzukuluzo chifukwa cha zolakwa za makolo awo.’+

  • Yesaya 48:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndidzabweza mkwiyo wanga chifukwa cha dzina langa,+ ndipo chifukwa cha ulemerero wanga, ine ndidzadziletsa kuti ndisakuwonongeni.+

  • Mika 7:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Kodi pali Mulungu winanso wofanana ndi inu+ amene amakhululukira zolakwa+ ndi machimo a anthu ake otsala omwe ndi cholowa chake?+ Inu simudzakhalabe wokwiya mpaka kalekale, pakuti kusonyeza kukoma mtima kosatha kumakusangalatsani.+

  • Nahumu 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Yehova sakwiya msanga+ ndipo ali ndi mphamvu zambiri,+ komatu Yehova salephera kulanga wolakwa.+

      Njira yake ili mumphepo yowononga ndi mumphepo yamkuntho. Mitambo ndilo fumbi lopondapo mapazi ake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena