Salimo 106:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Zikatero anali kukumbukira pangano limene anachita ndi iwo,+Ndipo anali kuwamvera chisoni chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwake kosatha.+
45 Zikatero anali kukumbukira pangano limene anachita ndi iwo,+Ndipo anali kuwamvera chisoni chifukwa cha kuchuluka kwa kukoma mtima kwake kosatha.+