Zekariya 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno mngelo amene anali kulankhula ndi ine uja anandiuza kuti: “Fuula kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Ndakhala ndikuchitira nsanje kwambiri Yerusalemu ndi Ziyoni.+ Zekariya 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova wa makamu+ wanena kuti: ‘Ziyoni ndidzam’chitira nsanje kwambiri.+ Ndidzam’chitira nsanje ndi kukwiya kwambiri.’”+
14 Ndiyeno mngelo amene anali kulankhula ndi ine uja anandiuza kuti: “Fuula kuti, ‘Yehova wa makamu wanena kuti: “Ndakhala ndikuchitira nsanje kwambiri Yerusalemu ndi Ziyoni.+
2 “Yehova wa makamu+ wanena kuti: ‘Ziyoni ndidzam’chitira nsanje kwambiri.+ Ndidzam’chitira nsanje ndi kukwiya kwambiri.’”+