Deuteronomo 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Malo alionse amene mapazi anu adzapondapo adzakhala anu.+ Malire a dziko lanu adzayambira kuchipululu kukafika ku Lebanoni, kuyambira ku mtsinje wa Firate, kukafika kunyanja ya kumadzulo.+ Deuteronomo 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anamuonetsanso dziko lonse la Nafitali, dziko la Efuraimu ndi la Manase, dziko lonse la Yuda mpaka kunyanja ya kumadzulo.+
24 Malo alionse amene mapazi anu adzapondapo adzakhala anu.+ Malire a dziko lanu adzayambira kuchipululu kukafika ku Lebanoni, kuyambira ku mtsinje wa Firate, kukafika kunyanja ya kumadzulo.+
2 Anamuonetsanso dziko lonse la Nafitali, dziko la Efuraimu ndi la Manase, dziko lonse la Yuda mpaka kunyanja ya kumadzulo.+