Hoseya 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Usasangalale iwe Isiraeli.+ Usachite zinthu mokondwera ngati mitundu ina ya anthu,+ pakuti wasiya Mulungu wako chifukwa cha dama.+ Ukukonda kulandira ndalama za uhule wako pamalo onse opunthira mbewu.+
9 “Usasangalale iwe Isiraeli.+ Usachite zinthu mokondwera ngati mitundu ina ya anthu,+ pakuti wasiya Mulungu wako chifukwa cha dama.+ Ukukonda kulandira ndalama za uhule wako pamalo onse opunthira mbewu.+