1 Mafumu 18:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Ahabu anauza Obadiya kuti: “Pita m’dzikoli, ukayendere akasupe onse a madzi ndi zigwa* zonse. Mwina tikhoza kupeza udzu wobiriwira+ woti tidyetse mahatchi ndi nyulu, kuti nyamazi zisapitirize kufa.”+ Yeremiya 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu otchuka atuma anthu wamba kukatunga madzi.+ Anthu wambawo afika kuzitsime koma sanapeze madzi.+ Abwerera ndi ziwiya zopanda kanthu. Achita manyazi+ ndipo akhumudwa moti aphimba mitu yawo.+
5 Ndiyeno Ahabu anauza Obadiya kuti: “Pita m’dzikoli, ukayendere akasupe onse a madzi ndi zigwa* zonse. Mwina tikhoza kupeza udzu wobiriwira+ woti tidyetse mahatchi ndi nyulu, kuti nyamazi zisapitirize kufa.”+
3 Anthu otchuka atuma anthu wamba kukatunga madzi.+ Anthu wambawo afika kuzitsime koma sanapeze madzi.+ Abwerera ndi ziwiya zopanda kanthu. Achita manyazi+ ndipo akhumudwa moti aphimba mitu yawo.+